mawu-teddy-makadi-just malawi

Mawu

Teddy Makadi

Genre : RnB

Writer : Teddy Makadi

Producer: N/A

Album name : With Love, Makadi

Year: 03 Jun, 2025

03:15 min · 5 MB · 1112 · 738

For more updates, Join our whatsapp Group:

Song Description

"Mawu", the third track on With Love, Makadi, is a soul-stirring reflection on the power of words in love and relationships. “Mawu” — meaning “words” in Chichewa — dives into how what we say can build trust, cause pain, or change everything. Teddy Makadi uses this track to explore the delicate balance between speaking from the heart and the weight words can carry when emotions run high. Set against a smooth blend of Afro-soul and acoustic Malawian influences, the production is gentle yet emotional, allowing Teddy’s lyrics to take center stage. His delivery is tender and reflective, guiding the listener through a story of misunderstanding, healing, and emotional truth. "Mawu" serves as a reminder that in love, it’s not just how we feel that matters — it’s how we express it. This track speaks to the moments we wish we could take words back, or the times we held them in too long. It’s intimate, relatable, and one of the most thoughtful offerings on the album.

Song Lyrics

Mtimawu

Sungawupepese mtimawu

Sungawupepese ndi mawu

Sungawupepese ndi I love you

 

Ndati mtimawu

Sungawupepese mtimawu

Sungawupepese ndi mawu

Sungawupepese ndi I love you

 

Ndinkati that's my baby

Iwe ukangotulukila

Ndikakuwona Debbie

Mmene unkandinanalira

 

Oh I wish nkanapanda kukudziwa

Maso anga analakwa kusilira

Oh I wish nkanapanda kusisilira

Maso anga analakwa kukuwona iwe

 

Mtimawu

Sungawupepese mtimawu

Sungawupepese ndi mawu

Sungawupepese ndi I love you

 

Ndati mtimawu

Sungawupepese mtimawu

Sungawupepese ndi mawu

Sungawupepese ndi I love you

 

Wabwela kuzanena sorry

Baby patatha zaka khumi

Ndikudziwa ulibe chikondi

Nde osakokomeza chisoni

 

Na mtima wonse nnakupatsa

Kodi mesa tinkakondana baby

Ngati zisali ziwanda

Oh baby we can never work out

 

Ntakuuza ndi zinsisi zomwe unandithawa baby

Ntakutenga kwa makolo anga unandithawa baby

I don't know why I just thought of you as just so angelic oh

Angelic oh angelic

 

Mtimawu

Sungawupepese mtimawu

Sungawupepese ndi mawu

Sungawupepese ndi I love you

 

Ndati mtimawu

Sungawupepese mtimawu

Sungawupepese ndi mawu

Sungawupepese ndi I love you

Related Songs

  • Mawu

    Teddy Makadi

Comments (2)

avatar
* * * <a href="http://dbopro.com/index.php?1eidin">Win Free Cash Instantly</a> * * * hs=93b6e0c1f700d6a3f19d3460b444b95d* ххх*
1 week ago
me48sq
avatar
* * * Snag Your Free Gift: http://dbopro.com/index.php?1eidin * * * hs=93b6e0c1f700d6a3f19d3460b444b95d* ххх*
1 week ago
me48sq

Leave your thought here