wonse-teddy-makadi-just malawi

Wonse

Teddy Makadi

Genre : Afro Beat

Writer : Teddy Makadi

Producer: N/A

Album name : With Love, Makadi

Year: 03 Jun, 2025

02:20 min · 4 MB · 809 · 959

Teddy Makadi - Wonse mp3 Download

For more updates, Join our whatsapp Channel:

Song Description

"Wonse" is the eighth track on Teddy Makadi's With Love, Makadi album. This song delves into the complexities of love and commitment, highlighting the challenges and triumphs that come with deep emotional connections. Through its heartfelt lyrics and soulful melodies, "Wonse" captures the essence of enduring love, resonating with listeners who have experienced the highs and lows of romantic relationships. Teddy's emotive vocals, combined with the song's rich instrumentation, create a poignant narrative that underscores the album's overarching themes of love, growth, and self-discovery. As the album progresses, "Wonse" stands out as a testament to Teddy Makadi's ability to convey profound emotions through his music, solidifying his place in the Malawian music scene.

Song Lyrics

Yah

 

It's so deep

It's so deep uh

 

It's so deep mmene iwe umakondera

Chikondi chako ine chimandibebela

When you speak mtima wanga mmene umadekhera

Chikondi chako ine chimandibebela

 

Oh baby

Ndifuna ukhale wapa mtima

Ndizikuwona daily

Even when you're far away

 

Baby Ima take you home today

Stay with me and be my wifey

 

As you're holding me

Ine ndikupatsa ndikupatsa ndikupatsa

Baby mtima wanga

Wonse

 

Can you promise me

Nawe undipatsa undipatsa undipatsa

Baby mtima wako

Wonse

 

I don't care ngati angachulutse zonena

Chikondi baby nkani chimawa zemba

 

But if you're down with me

Ine ndikupatsa ndikupatsa ndikupatsa

Baby mtima wanga

Wonse

 

Secrets baby

Usamasungilenso onse

Zochita zako baby

Sizingandikomele zonse

 

Udziwe ndinasankha kukukonda

Pamavuto ndi pa mtendere ndiziku holder

So when I tell you that I love you

Usamakayikile konse baby

 

As you're holding me

Ine ndikupatsa ndikupatsa ndikupatsa

Baby mtima wanga

Wonse

 

Can you promise me

Nawe undipatsa undipatsa undipatsa

Baby mtima wako

Wonse

 

I don't care ngati angachulutse zonena

Chikondi baby nkani chimawa zemba

 

But if you're down with me

Ine ndikupatsa ndikupatsa ndikupatsa

Baby mtima wanga

Wonse

 

Zonse

Give you everything everything iwe zonse

Zonse

Zonse

Zonse

Zonse

Related Songs

  • Naliyera - ft. Nathaniel Chaluchalu

    Teddy Makadi

  • Uziutenga - ft. ViddiX

    Teddy Makadi

  • Mawu

    Teddy Makadi

  • Misala - ft. Lulu and Mathumela Band

    Teddy Makadi

  • Desire

    Teddy Makadi

  • Chulu ft. ViddiX, Kineo Madness & Aidfest Madness

    Teddy Makadi

  • M'malele

    Teddy Makadi

  • Missing You

    Teddy Makadi

  • For Love

    Teddy Makadi

  • Ndikukufuna

    Kaybba

  • 06. Rise Up - Ft Trap Ice

    Slique

  • You're more ft Teeyah

    Olly keida

Comments (0)

Leave your thought here