Genre : Hip Hop
Writer : Bono Bonongwe & Prince Sparta
Producer: D Wine
Album name : Single
Year: 29 Oct, 2023
02:51 min · 8 MB · 1076 · 2.2k
Ukumwa Kuposa Bayala Song By Bono Bonogwe & Prince Sparta,Stream,Download & Enjoy
Asaaa
Bono Bonongwe, baby
yeah
ayayayayaaaah
yah
iwe ase ndadabwa nazo
mene ukusipila
mene botolo ukutsitsila
uchita kukhala ngati ukulipila
chosecho umadikila zoti nzikugulila
mene ukusipila
mene botolo ukutsitsila
uchita kukhala ngati ukulipila
chosecho umadikila zoti nzikugulila
ukumwa kuposa bayala
ukumwa kuposa bayala
ukumwa kuposa bayala
kuposa bayala
ukumwa kuposa bayala (gwe)
ukumwa kuposa bayala
ukumwa kuposa bayala
ukumwa kuposa bayala
kuposa bayala
ukumwa kuposa bayala
iwe ase ukuiyendetsa bwanji gist
ndili bottle number 3 uli bottle number 6
abraz please mundiphetsa ndima bills
umenewo ukatha basi tidye ma chills
yah, ukumwa ngati ukukaimba
bill yanga ukuitanitsaso Breezer
amwene nsakumwetseni ngati inuyo ndi Linda
komaso botolo mukumwalo nde mulipila (Bono Bonongwe! )
mowa ogula ine, mpaka kuika status ati lelo tigona panja
komaso ukungojambula zithuzi, ufuna ukapita kwanuko akakutame ndindani? (Ehe!)
shot ya Tequila mpaka ku dabula (Ehe!)
ukuitana anzako ngati ugula (Ehe!)
ndikungokuona sindikuyankhula (Ehe!)
amwene inuyo mwamasuka
iwe ase ndadabwa nazo
mene ukusipila
mene botolo ukutsitsila
uchita kukhala ngati ukulipila
chosecho umadikila zoti nzikugulila
mene ukusipila
mene botolo ukutsitsila
uchita kukhala ngati ukulipila
chosecho umadikila zoti nzikugulila
ukumwa kuposa bayala
ukumwa kuposa bayala
ukumwa kuposa bayala
kuposa bayala
ukumwa kuposa bayala (gwe)
ukumwa kuposa bayala
ukumwa kuposa bayala
ukumwa kuposa bayala
kuposa bayala
ukumwa kuposa bayala
ukumwa kuposa bayala
ukumwa kuposa bayala
ukumwa kuposa bayala
kuposa bayala
ukumwa kuposa bayala
ukumwa kuposa bayala
ukumwa kuposa bayala
ukumwa kuposa bayala
kuposa bayala
ukumwa kuposa bayala
Comments (1)