Genre : Afro Soul
Writer : Mr B
Producer: N/A
Album name : Single
Year: 06 Dec, 2025
Duration: 08:00 min · File size: 8 MB · Downloads: 18 · Plays: 132
Mr B - Komwe Tachoka mp3 Download
Stream & Download "Komwe Tachoka"
Lyrics (Chichewa with English Translation)
(Music starts with a standout guitar tune, followed by the entry of the drums)
(Verse 1)
Ndikuti kwawo,ndi ku Mulanje
Mkazi wokongola,mtima wake ndi wolemera
Anasiya mapiri a tea,anatsata mtima wake
Kukhala wanga,ngakhale ndinalibe kanthu
Translation:
Away from home,in Mulanje
A beautiful woman,with a heart so rich
She left the tea mountains,she followed her heart
To her man,even though I had nothing
(Chorus)
Koma muchikondi tidagwirana manja
Tidakhala mu ka room kophaphatiza,ife pawuwiri pathu basi
Timadzilimbikitsa,kuti tsiku lina tidadziwa
Kuti moyo wathu udzasintha,powona Komwe tachoka
Translation:
But we held onto love,hand in hand
We lived in a small room,just the two of us
We persevered,we knew one day
That our life would blossom,from where we came from
(Verse 2)
Ku dziko la eni,kunja kwa Malawi
Mtendele onse tinawusiya,kundikonabe ngakhale
Sitinali ndi zinthu,koma timadalira thanzi lathu
Chimwemwe chathu chidali chosatha,mukaroom kophaphatiza momwemo
Translation:
In a foreign land,outside Malawi
She left all comforts,for my sake
We had no luxury things,but we relied on our bond
Our happiness was endless,in that very room
(Chorus)
Koma muchikondi tidagwirana manja
Tidakhala mu ka room kophaphatiza,ife pawuwiri pathu basi
Timadzilimbikitsa,kuti tsiku lina tidadziwa
Kuti moyo wathu udzasintha,powona Komwe tachoka
(Bridge)
Pamene zinthu sizimayenda, koma Ife sitidasoke!
Mwayi udatseguka,m’dalitso unatigwela.
Tidakwatirana m’chikondi,ndipo lero tili pamodzi muchikondi
Tikumanga nyumba yathu,ya kumaloto, ku Lilongwe!
Translation:
That's where the witch tried to destroy us…but we were not shaken!
Opportunity opened up,before our very eyes
We married in love,and today we are together
We are looking at our house,our dream house, in Lilongwe!
(Guitar Solo)
(The standout guitar tune returns, more powerful and emotional now, telling the story of the struggle and the triumph without words. The drums continue their strong, celebratory rhythm underneath.)
(Chorus - More Uplifting and Powerful)
Pamene love tagwirana manja!
Sitikukumbukanso zaka room kophatiza,ife awiri basi!
Tidalimbikitsana,tsiku lalelo tadala!
Lero moyo wathu wasintha,kuyangana Komwe tachoka!
Translation:
When we held onto love,hand in hand!
We no longer remember the small room,just the two of us!
We persevered,one day we rejoiced!
Today our life has blossomed,from where we came from!
(Outro)
Komwe tachoka…eehee
Komwe tachoka…Mulanje, Cape Town to Lilongwe
Komwe tachoka…tikuyamika
Zikomo,Ambuye… Zikomo, mtima wako, mkazi wanga. Ndiwe mai Malawi
Translation:
Where we came from…yes
Where we came from…from Mulanje, to Lilongwe
Where we came from…we are grateful
Thank you,Lord… Thank you for your heart, my wife.
(Music fades out with the gentle guitar riff and the soft, fading beat of the drum)
---
Artist: Mr. B
Comments (0)